Exodus 1:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma azambawo ankaopa Mulungu, kotero kuti mau a mfumu aja sadaŵasamale konse, ana aamunawo ankangoŵaleka amoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anamwino anaopa Mulungu, ndipo sanachite monga mfumu ya Aejipito inawauza, koma analeka ana amuna akhale ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma azambawo ankaopa Mulungu ndipo sanachite zimene mfumu ya Igupto inawawuza kuti achite. Iwo analeka ana aamuna kuti akhale ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anamwino anaopa Mulungu, ndipo sanacita monga mfumu ya Aigupto inawauza, koma analeka ana amuna akhale ndi moyo.