Exodus 1:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu ija idaŵaitana azamba aja niŵafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwaŵaleka ana aamuna osaŵapha?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu ya Aejipito inaitana anamwino, ninena nao, Mwachita ichi chifukwa ninji, ndi kuleka ana amunawo akhale ndi moyo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mfumu ya Igupto inayitanitsa azamba aja ndi kuwafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwachita zimenezi? Bwanji mwasiya ana aamuna kuti akhale ndi moyo?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu ya Aigupto inaitana anamwino, ninena nao, Mwacita ici cifukwa ninji, ndi kuleka ana amunawo akhale ndi moyo?