Exodus 1:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Mulungu adaŵakomera mtima azambawo, mwakuti Aisraele adapitirirabe kuchulukana, nakhala amphamvu kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero Mulungu anawachitira zabwino anamwino; ndipo anthuwo anachuluka, nakhala nazo mphamvu zazikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Mulungu anawakomera mtima azambawo, ndipo Aisraeli anapitirirabe kuchulukana nakhala amphamvu kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero Mulungu anawacitira zabwino anamwino; ndipo anthuwo anacuruka, nakhala nazo mphamvu zazikuru.