Exodus 1:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono chifukwa choti azambawo ankaopa Mulungu, Mulungu adaŵapatsa mabanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunatero kuti, popeza anamwino anaopa Mulungu, Iye anawamangitsira mabanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti azambawo ankaopa Mulungu, Iye anawapatsa mabanja awoawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunatero kuti, popeza anamwino anaopa Mulungu, iye anawamangitsira mabanja.