Exodus 10:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta adaumitsa Farao mtima, ndipo sadalole kuti anthuwo apite.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova analimbitsa mtima wake wa Farao, ndipo anakana kuwaleka amuke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova anawumitsa mtima wa Farao ndipo sanafune kuwalola kuti apite.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova analimbitsa mtima wace wa Farao, ndipo anakana kuwaleka amuke.