Exodus 10:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Farao adaitananso Mose ndi Aroni naŵauza kuti, “Pitani mukapembedze Chauta, Mulungu wanu. Koma tsono apite ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawabwereretsa Mose ndi Aroni kwa Farao, nanena nao, Mukani, katumikireni Yehova Mulungu wanu. Koma amene adzapitawo ndiwo yani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Mose ndi Aaroni anayitanidwanso kwa Farao ndipo anati, “Pitani kapembedzeni Yehova Mulungu wanu. Koma ndani amene adzapite?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawabwereretsa Mose ndi Aroni kwa Farao, nanena nao, Mukani, katumikireni Yehova Mulungu wanu. Koma amene adzapitawo ndiwo ani?