Exodus 12:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalankhula kwa Mose ndi Aroni m'dziko lija la Ejipito kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni m'dziko la Ejipito, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anayankhula kwa Mose ndi Aaroni mʼdziko la Igupto kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni m'dziko la Aigupto, ndi kuti,