Exodus 12:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musasiyeko nyama ina mpaka m'maŵa, motero ina ikatsalako, muitenthe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo musasiyako kufikira m'mawa; koma yotsalira kufikira m'mamawayo muipsereze ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musadzasiye nyama ina mpaka mmawa, ngati ina idzatsala mpaka mmawa, mudzayitenthe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo musasiyako kufikira m'mawa; koma yotsalira kufikira m'mawayo muipsereze ndi moto: