Exodus 12:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adati, “Muzidzadya buledi wosafufumitsa pa masiku asanu ndi aŵiri. Pa tsiku loyamba muzidzachotsa zotupitsira buledi m'nyumba zanu zonse, chifukwa pa masiku asanu ndi aŵiri aliyense wodya buledi wofufumitsa adzachotsedwa pakati pa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku asanu ndi awiri muzidya mkate wopanda chotupitsa; lingakhale tsiku loyamba muzichotsa chotupitsa m'nyumba zanu; pakuti aliyense wakudya mkate wa chotupitsa kuyambira tsiku loyamba kufikira tsiku lachisanu ndi chiwiri, munthu amene adzasadzidwa kwa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa masiku asanu ndi awiri muzidya buledi wopanda yisiti. Tsiku loyamba muzichotsa yisiti mʼnyumba zanu, ngati aliyense adzadya kanthu kalikonse kali ndi yisiti kuyambira tsiku loyamba mpaka tsiku lachisanu ndi chiwiri, munthu ameneyo adzayenera kuchotsedwa mʼgulu la Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku asanu ndi awiri muzidya mkate wopanda cotupitsa; lingakhale tsiku loyamba muzicotsa cotupitsa m'nyumba zanu; pakuti ali yense wakudya mkate wa cotupitsa kuyambira tsiku loyamba kufikira tsiku lacisanu ndi ciwiri, munthu amene adzasadzidwa kwa Israyeli.