Exodus 12:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mwezi uno udzakhala mwezi wanu woyambira chaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwezi uno uzikhala kwa inu woyamba wa miyezi; muziuyesa mwezi woyamba wa chaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mwezi uno uzikhala mwezi wanu woyamba wa chaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwezi uno uzikhala kwa inu woyamba wa miyezi; muziuyesa mwezi woyamba wa caka.