Exodus 12:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muziŵamvera malamulo ameneŵa inuyo ndi ana anu mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muzisunga chinthu ichi chikhale lemba la kwa inu, ndi kwa ana anu ku nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Muzimvera malamulo amenewa kwa muyaya, inu ndi zidzukulu zanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muzisunga cinthu ici cikhale lemba la kwa inu, ndi kwa ana anu ku nthawi zonse.