Exodus 12:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele adakhalako zaka 430 ku Ejipito kuja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kukhala kwa ana a Israele anakhala m'Ejipito ndiko zaka mazana anai kudza makumi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Aisraeli anakhala ku Igupto kwa zaka 430.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kukhala kwa ana a Israyeli anakhala m'Aigupto ndiko zaka mazana anai kudza makumi atatu.