Exodus 12:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kapolo aliyense wochita kugulidwa angadyeko, koma atayamba waumbalidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma kapolo wa mwini aliyense, wogula ndi ndalama, utamdula, ndipo adyeko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kapolo aliyense amene munagula angadye ngati atayamba wachita mdulidwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma kapolo wa mwini ali yense, wogula ndi ndarama, utamdula, ndipo adyeko.