Exodus 13:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musunge malangizo ameneŵa pa nthaŵi yake chaka ndi chaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake uzikasunga lemba ili pa nyengo yake chaka ndi chaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muzichita mwambo uwu pa nthawi yake chaka ndi chaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace uzikasunga lemba ili pa nyengo yace caka ndi caka.