Exodus 13:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimenechi chidzakhala chikumbutso, monga ngati chizindikiro chomangidwa pa dzanja lanu kapena pamphumi panu, chifukwa Chauta adatitulutsa ku Ejipito ndi dzanja lake lamphamvu.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chizikhala ngati chizindikiro pa dzanja lako, ndi chapamphumi pakati pa maso ako; pakuti Yehova anatitulutsa m'Ejipito ndi dzanja lamphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo chidzakhala kwa inu ngati chizindikiro chomangidwa pa dzanja lanu ndi pamphumi panu kuonetsa kuti Yehova anakutulutsani mʼdziko la Igupto ndi dzanja lake lamphamvu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cizikhala ngati cizindikilo pa dzanja lako, ndi capamphumi pakati pa maso ako; pakuti Yehova anatiturutsa m'Aigupto ndi dzanja lamphamvu.