Exodus 13:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzidzadya buledi wosafufumitsa pa masiku asanu ndi aŵiri. Pasamadzakhala buledi wofufumitsa, kapena chofufumitsira chilichonse m'dziko lanu lonselo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Azikadya mkate wopanda chotupitsa masiku asanu ndi awiriwo ndipo kasaoneke kanthu ka chotupitsa kwanu; inde chotupitsa chisaoneke kwanu m'malire ako onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudye buledi wopanda yisiti masiku asanu ndi awiri. Pasapezeke chinthu chilichonse chokhala ndi yisiti pakati panu, kapena paliponse mʼdziko lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Azikadya mkate wopanda cotupitsa masiku asanu ndi awiriwo ndipo kasaoneke kanthu ka cotupitsa kwanu; inde cotupitsa cisaoneke kwanu m'malire ako onse.