Exodus 14:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adafunsa Mose kuti, “Kodi nchifukwa chakuti ku Ejipito kunalibe malo a manda, kuti inuyo mutifikitse kuchipululu kuno kuti tidzafe? Mwatichita chiyani potitulutsa ku Ejipito?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa Mose, Kodi mwatichotsera kuti tikafe m'chipululu chifukwa panalibe manda m'Ejipito? Nchiyani ichi mwatichitira kuti mwatitulutsa m'Ejipito?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anafunsa Mose kuti, “Kodi nʼchifukwa chakuti kunalibe manda ku dziko la Igupto kuti iwe utibweretse muno mʼchipululu kuti tidzafe? Chimene watichitachi nʼchiyani, kutitulutsa mʼdziko la Igupto?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa Mose, Kodi mwaticotsera kuti tikafe m'cipululu cifukwa panahbe manda m'Aigupto? Nciani ici mwaticitira kuti mwatiturutsa m'Aigupto?