Exodus 14:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tenga ndodo yakoyo, ndipo utambalitse dzanja pa nyanja, kuigaŵa nyanjayo kuti Aisraele aoloke pouma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwe nyamula ndodo yako, nutambasulire dzanja lako kunyanja, nuigawe, kuti ana a Israele alowe pakati pa nyanja pouma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyamula ndodo yako ndi kutambasula dzanja lako kuloza ku nyanja, kugawa madzi kuti Aisraeli awoloke powuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwe nyamula ndodo yako, nutambasulire dzanja lako kunyanja, nuigawe, kuti ana a Israyeli alowe pakati pa nyanja pouma.