Exodus 14:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Farao adzaganiza kuti, ‘Aisraele asokonezeka, akungoyendayenda m'dzikomo, azingidwa ndi chipululu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Farao adzanena za ana a Israele, Azimidwa dziko, chipululu chawatsekera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Farao adzaganiza kuti ‘Aisraeli asokonezeka nʼkumangozungulirazungulira mu dzikomo, chipululu chitawazinga.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Farao adzanena za ana a Israyeli, Azimidwa dziko, cipululu cawatsekera.