Exodus 14:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Farao adakonzetsa galeta lake lankhondo, ndipo adauza asilikali ake kuti apite naye limodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamanga galeta lake, napita nao anthu ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anakonzetsa galeta lake ndipo ananyamuka pamodzi ndi ankhondo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamanga gareta lace, napita nao anthu ace;