Exodus 15:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu mudangouzira ndi mphepo yanu, ndipo nyanja idaŵamiza. Adangomira ngati chitsulo mpaka pansi pa madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munaombetsa mphepo yanu, nyanja inawamiza; anamira m'madzi aakulu ngati mtovu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu munawuzira mphepo yanu, ndipo nyanja inawaphimba. Iwo anamira ngati chitsulo mʼmadzi amphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munaombetsa mphepo yanu, nyanja inawamiza; Anamira m'madzi akuru ngati mtobvu.