Exodus 15:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inu Chauta, kodi pali mulungu wina wofanafana nanu? Ndani amafanafana ndi Inu, amene muli aulemu chifukwa cha ungwiro wanu? Ndani amafanafana nanu, Inu amene muli oopsa chifukwa cha ntchito zanu zaulemu ndi zodabwitsa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Afanana ndi Inu ndani mwa milungu, Yehova? Afanana ndi Inu ndani, wolemekezedwa, woyera, woopsa pomyamika, wakuchita zozizwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithu Yehova, pakati pa milungu, ndani afanana nanu? Inu amene muli woyera, ndiponso wotamandika wolemekezeka, chifukwa cha ntchito zanu, zazikulu ndi zodabwitsa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Manana ndi Inu ndani mwa milungu, Yehova? Manana ndi Inu ndani, wolemekezedwa, woyera, Woopsa pomyamika, wakucita zozizwa?