Exodus 15:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma anthu amene mudaŵaombola, mudaŵatsogolera ndi chikondi chanu chosasinthika. Mudaŵatsogolera ku malo anu oyera ndi mphamvu zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa chifundo chanu mwatsogolera anthu amene mudawaombola; mwamphamvu yanu mudawalondolera njira yakunka pokhala panu poyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi chikondi chanu chosasinthika mudzatsogolera anthu amene munawawombola. Ndi mphamvu zanu munawatsogolera ku malo anu woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa cifundo canu mwatsogolera anthu amene mudawaombola; Mwa mphamvu yanu mudawalondolera njira yakumka pokhala panu poyera.