Exodus 15:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a mitundu ina amva mbiriyi, ndipo anjenjemera ndi mantha. Mantha oopsa aŵagwira Afilisti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mitundu ya anthu idamva, inanthunthumira; kuda mtima kwagwira anthu okhala m'Filistiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amitundu ina anamva za mbiriyi ndipo ananjenjemera ndi mantha, mantha woopsa agwira anthu a dziko la Filisiti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mitundu ya anthu idamva, inanthunthumira; Kuda mtima kwagwira anthu okhala m'Filistiya.