Exodus 15:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzakhala mfumu mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adzachita ufumu nthawi yonka muyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova adzalamula mpaka muyaya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adzacita ufumu nthawi yomka muyaya.