Exodus 15:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Miriyamu adaŵaimbira iwowo nyimbo yakuti, “Imbirani Chauta chifukwa wapambana, waponya m'nyanja akavalo pamodzi ndi okwerapo ake omwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Miriyamu anawayankha, Imbirani Yehova, pakuti wapambanatu; kavalo ndi wokwera wake anawaponya m'nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Miriamu anawayimbira nyimbo iyi: “Imbirani Yehova, chifukwa iye wapambana. Kavalo ndi wokwerapo wake Iye wawamiza mʼnyanja.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Miriamu anawayankha, Yimbirani Yehova, pakuti wapambanatu; Kavalo ndi wokwera wace anawaponya m'nyanja. Madzi a ku Mara.