Exodus 15:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo anthu aja adadandaulira Mose, namufunsa kuti, “Kodi ife timwa chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu anadandaulira Mose, ndi kuti, Tidzamwa chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anthu aja anadandaulira Mose ndi kumufunsa kuti, “Kodi tikumwa chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu anadandaulira Mose, ndi kuti, Tidzamwa ciani?