Exodus 15:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adakafika ku Elimu kumene kunali akasupe khumi ndi aŵiri, ndi mitengo ya migwalangwa makumi asanu ndi aŵiri. Tsono adamanga mahema ao kumeneko pafupi ndi madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anafika pa Elimu, ndi pamenepo panali akasupe a madzi khumi ndi awiri, ndi akanjedza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamanga chigono chao pomwepo pa madziwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anafika ku Elimu, kumene kunali akasupe khumi ndi awiri ndi mitengo ya migwalangwa makumi asanu ndi awiri, ndipo anamanga misasa yawo kumeneko pafupi ndi madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anafika pa Elimu, ndi pamenepo panali akasupe a madzi khumi ndi awiri, ndi akanjedza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamanga cigono cao pomwepo pa madziwo.