Exodus 15:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumagonjetsa adani anu ndi ulemerero wanu wopambana. Ukali wanu woyaka ngati moto ukuŵatentha ngati mapesi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndi ukulu wanu waukulu mwapasula akuukira Inu; mwatumiza mkwiyo wanu, unawanyeketsa ngati chiputu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi ulemerero wanu waukulu, munagonjetsa okutsutsani. Inu munatumiza mkwiyo wanu waukulu; ndipo unawapsereza ngati udzu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndi ukulu wanu waukuru mwapasula akuukira Inu; Mwatumiza mkwiyo wanu, unawanyeketsa ngati ciputu.