Exodus 15:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mutauzira mpweya wanu, madzi adaunjikana pa malo amodzi. Madzi oyenda adangoima kuti chilili, ngati khoma. Nyanja yozamayo idalimba mpaka pansi pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndi mpumo wa m'mphuno mwanu madzi anaunjikika, mayendedwe ake anakhala chilili ngati mulu; zozama zinalimba m'kati mwa nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mpweya wotuluka mʼmphuno mwanu madzi anawunjikana pamodzi. Nyanja yakuya ija inasanduka madzi owuma gwaa kufika pansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipondi mpumo wa m'mphuno mwanu madzi anaunjikika, Mayendedwe ace anakhala ciriri ngati mulu; Zozama zinalimba m'kati mwa nyanja.