Exodus 16:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lachisanu ndi chiŵirilo anthu ena adaapita kuti akatole chakudya, koma sadachipeze.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali tsiku la Sabata, kuti anthu ena anatuluka kukaola, koma sanaupeze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe anthu ena anapita kuti akatole chakudya tsiku lachisanu ndi chiwiri, koma sanapeze kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali tsiku la Sabata, kuti anthu ena anaturuka kukaola, koma sanaupeza.