Exodus 16:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu sankagwira ntchito pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu anapumula tsiku lachisanu ndi chiwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anthu anapuma tsiku lachisanu ndi chiwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu anapumula tsiku lacisanu ndi ciwiri.