Exodus 16:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe Chauta adalamulira Mose, Aroni adaika mtsukowo patsogolo pa bokosi lachipangano, kuti manayo asungike.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga Yehova anauza Mose, momwemo Aroni anauika patsogolo pa Mboni, usungikeko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe Yehova analamulira Mose, Aaroni anayika mtsuko uja pafupi ndi bokosi la Chipangano kuti manawo asungike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga Yehova anauza Mose, momwemo Aroni anauika patsogolo pa Mboni, usungikeko.