Exodus 18:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yetero adabweranso ndi ana aamuna aŵiri aja a Zipora. Mwana woyamba Mose adaamutcha Geresomo (chifukwa adati, “Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo.”)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
dzina la winayo ndiye Geresomo, pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko lachilendo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mwana wake wamkaziyo pamodzi ndi ana ake aamuna awiri. Mose anamupatsa mwana wachisamba dzina loti Geresomu popeza anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
dzina la winayo ndiye Gerisomu, pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko lacilendo;