Exodus 18:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wina adakauza Mose kuti, “Mpongozi wanu Yetero akubwera ndi mkazi wanu ndi ana anu aŵiri aamuna.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati kwa Mose, Ine mpongozi wako Yetero ndadza kwa iwe, ndi mkazi wako, ndi ana ake omwe awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yetero anali atatumiza uthenga kwa Mose kuti, “Ine Yetero, mpongozi wako, ndikubwera ndi mkazi wako ndi ana ake awiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati kwa Mose, Ine mpongozi wako Yetero ndadza kwa iwe, ndi mkazi wako, ndi ana ace omwe awiri.