Exodus 19:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka Mose adaŵauza kuti, “Mkucha uno, mukonzeke. Musayandikize mkazi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa anthu, Mukonzekeretu tsiku lachitatu nimusayandikiza mkazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka iye anati kwa anthu, “Konzekerani tsiku lachitatu, musagone pamodzi ndi mkazi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa anthu, Mukonzekeretu tsiku lacitatu nimusayandikiza mkazi.