Exodus 19:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adaŵatsogolera anthuwo kuchoka kumahemako, kuti akakumane ndi Mulungu, ndipo onsewo adaima patsinde pa phiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anatulutsa anthu kutsasa, kuti akomane ndi Mulungu; ndipo anaima patsinde pa phiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mose anatsogolera anthu kutuluka mʼmisasa kukakumana ndi Mulungu, ndipo anayima mʼmunsi mwa phiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anaturutsa anthu kutsasa, kuti akomane ndi Mulungu; ndipo anaima patsinde pa phiri.