Exodus 19:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adauza Moseyo kuti, “Tsika pansi, ndipo ukamtenge Aroni, ubwere naye kuno. Koma ansembe pamodzi ndi anthu asabzole malirewo kubwera kwa Ine kuno, kuti ndingadzaŵalange.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati kwa iye, Muka, tsika; nukwere iwe ndi Aroni pamodzi ndi iwe; koma ansembe ndi anthu asapyole kukwera kwa Yehova, angawapasule.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anayankha, “Tsika ukamutenge Aaroni. Koma ansembe ndi anthu asayesere kubzola malire kuti abwere kwa Yehova chifukwa Iye adzawalanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati kwa iye, Muka, tsika: nukwere iwe ndi Aroni pamodzi ndi iwe; koma ansembe ndi anthu asapyole kukwera kwa Yehova, angawapasule.