Exodus 19:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Mose adakaitana atsogoleri a Aisraele, ndipo adaŵauza zonse zimene Chauta adamlamula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anadza, naitana akulu a anthu, nawaikira pamaso pao mau awa onse amene Yehova adamuuza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mose anabwerera ndi kuyitanitsa akuluakulu. Atabwera anawafotokozera mawu amene Yehova anamulamulira kuti adzanene.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anadza, naitana akuru a anthu, nawaikira pamaso pao mau awa onse amene Yehova adamuuza.