Exodus 2:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atsikana atabwerera kwa bambo wao Reuele, bambo waoyo adaŵafunsa kuti, “Bwanji mwabwerako msanga chotere lero?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mene anafika kwa Reuwele atate wao, iye anati, Mwabwera msanga bwanji lero?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atsikana aja atabwerera kwa abambo awo Reueli, iye anawafunsa kuti, “Chifukwa chiyani lero mwabwera msanga?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mene anafika kwa Rehueli atate wao, iye anati, Mwabwera msanga bwanji lero?