Exodus 2:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Mose adavomera kukhala nao komweko, ndipo Reuele adapatsa Moseyo mwana wake Zipora kuti akhale mkazi wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anavomera kukhala naye munthuyo; ndipo anampatsa Mose mwana wake wamkazi Zipora.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anavomera kukhala ndi Reueli, ndipo anamupatsa Zipora kuti akhale mkazi wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anabvomera kukhala naye munthuyo; ndipo anampatsa Mose mwana wace wamkazi Zipora.