Exodus 2:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adamva kudandaula kwaoko, nakumbukira chipangano chake chija chimene adachita ndi Abrahamu, Isaki ndi Yakobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mulungu anamva kubuula kwao, ndi Mulungu anakumbukira chipangano chake ndi Abrahamu, ndi Isaki, ndi Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu anamva kubuwula kwawo ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abrahamu, Isake ndi Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Molungu anamva kubuula kwao, ndi Mulungu anakumbukila cipangano cace ndi Abrahamu, ndi Isake, ndi Yakobo.