Exodus 20:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu ankaima kutali, Mose yekha ndiye adayandikira mtambo wamdima m'mene munali Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu anaima patali, koma Mose anayandikiza ku mdima waukulu kuli Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu aja anayima patali koma Mose anayandikira mtambo wakuda kumene kunali Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu anaima patali, koma Mose anayandikiza ku mdima waukuru kuli Mulungu.