Exodus 20:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popita ku guwa langa, musadzaponde pa makwerero, kuti maliseche anu angaonekere.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena usakwere ndi makwerero ku guwa langa la nsembe, kuti angaoneke maliseche ako pamenepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musamakwere pa makwerero popita pa guwa langa lansembe kuti mungaonetse maliseche anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena usakwere ndi makwerero ku guwa langa la nsembe, kuti angaoneke marisece ako pamenepo.