Exodus 20:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masiku asanu ndi limodzi uzigwira ntchito zako zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku asanu ndi limodzi uzigwira, ndi kumaliza ntchito zako zonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uzigwira ntchito zako zonse masiku asanu ndi limodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku asanu ndi limodzi uzigwira, ndi kumariza nchito zako zonse;