Exodus 21:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akakwatira mkazi wina, ayenera kupitirira kumpatsa woyambayo chakudya ndi zovala. Azimlolanso zonse zomuyenera ngati mkazi wake, monga ankachitira kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akamtengera mkazi wina, asachepetse chakudya chake, zovala zake, ndi za ukwati zakezake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati akwatira mkazi wina, asamumane woyambayo chakudya ngakhale chovala ndipo apiritirize kugona naye ngati mkazi wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akamtengera mkazi wina, asacepetse cakudya cace, zobvala zace, ndi za ukwati zace zace.