Exodus 21:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akapanda kumchitira zimenezi, ammasule kuti akhale mfulu, koma osalandirapo ndalama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akapanda kumchitira izi zitatu, azituluka chabe, osaperekapo ndalama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati sangathe kumuchitira zonsezi, ndiye amuleke apite popanda kulipira kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akapanda kumcitira izi zitatu, azituruka cabe, osaperekapo ndalama.