Exodus 21:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu aliyense amene amenya bambo wake kapena mai wake, aphedwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu wakukantha atate wake, kapena amai wake, aphedwe ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munthu aliyense amene amenya abambo ake kapena mayi ake ayenera kuphedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthuwakukanthaatatewace, kapena amai wace, aphedwe ndithu.