Exodus 21:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu akamenyana, ndipo wina mwa iwowo amenya mnzake ndi mwala kapena nkhonya, koma osamupha mnzakeyo, munthu womenyedwayo akadwala nakagona pa bedi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akalimbana amuna, ndipo wina akakantha mnzake ndi mwala, kapena ndi nkhonya, wosafa iye, koma wakhulungira pakama;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati anthu awiri akangana ndipo wina amenya mnzake ndi mwala kapena nkhonya koma wosamupha, womenyedwayo akadwala nagona pa bedi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akalimbana amuna, ndipo wina akakantha mnzace ndi mwala, kapena ndi nkhonyo, wosafa iye, koma wakhulungira pakama;