Exodus 21:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma maiyo akampweteka, chilango chake chidzakhala chotere: moyo kulipa moyo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati kuphweteka kukalipo, uzipereka moyo kulipa moyo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati wavulazidwa kwambiri, ndiye malipiro ake adzakhala motere: moyo kulipa moyo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati kuphweteka kukalipo, uzipereka moyo kulipa moyo,